Pologalamu yapadera pa mau a ArkiEpiskopi Thomas Luke Msusa

Pologalamu yapadera imene Bambo Joseph Kimu akuthilira ndemanga pa mau amphamvu, ofunika komanso aluntha okhudza mmene tingasankhire atsogoleri athu adziko amene adalankhulidwa ndi  Ambuye Thomas Luke Msusa, ArkiEpiskop wa Archdayosizi ya Blantyre, loweruka pa 07, July, 2018,pambuyo  pa mwambo wodzodza ansembe khumi ndi mmodzi. Uthenga wa Ambuye Thomas Luke Msusa ena authanthauzira mosiyina ndi mmene uthengawo unayenera kutanthauza. Radio Maria ikufuna kutiongolera m’mene uthengawu unayenera kutanthauzira.Current track

Title

Artist