KODI NDIBWINO KUYEREKEZA NDALE ZA KU MALAWI NDI NSINKHU WA PAPA FRANCISCO YEMWE NDI MTSOGOLERI WA MPINGO WA KATOLIKA PA DZIKO LONSE LAPANSI?

Rev. Fr. Joseph Kimu

KODI NDIBWINO KUYEREKEZA NDALE ZA KU MALAWI NDI NSINKHU WA PAPA FRANCISCO YEMWE NDI MTSOGOLERI WA MPINGO WA KATOLIKA PA DZIKO LONSE LAPANSI?

Mupologalamuyi muli verani zomwe adalankhula mkulu wina pa nsonkhano wa chipani zomwe mwanjira ina nzonyoza Papa komanso zosasangalatsa akatolika.

Mverani Radio Maria Malawi nthawi zonse!
Thandizani Radio Maria Malawi nthawi zonse!
Liu Lachikhristu M’nyumba Mwanu!Current track

Title

Artist