Kodi Masakalamentalia akale kapena akutha tingawasunge bwanji?

Rev. Fr. Petros Mwale

Mu pologalamu ino Bambo Petros Mwale , Wansembe kuchokera ku Dayosizi ya Mzuzu akutithandiza kumvetsa kufunikira kwa Masakalamentalia monga ma kolona ndinso mmene tingasungire zinthu zimenezi pamene zatha, monga pamene zaduka.Current track

Title

Artist