Kodi Episkop(Bishop) amasankhidwa bwanji?

Rev. Fr. Petros Mwale

Maphunziro ofunikira kwambiri othandiza kudziwa mmene Apapa amachitira pofuna kusankha Episikopi kapena kuti Bishop.

Bambo Petros Mwale, wansembe wochokera ku Mzuzu Diocese kutambasula tsatanetsatane komanso dongolo la kasankhidwe ka Episkop(Bishop) komanso ntchito zakeCurrent track

Title

Artist