Events

Nthenda ya Ebola, akuti ikupitilirabe kufala mmadera osiyanasiyana m’dziko la Democratic Republic of Congo (DRC). Malingana ndi malipoti a wailesi ya BBC, nduna ya za umoyo m’dzikomo yati pali mantha oti nthendayi itha kufika poipa kwambiri zomwe zingapangitse kuti pakhale povuta kuthana nayo. Iyo yati m’dzinda wa Mbandaka ndi womwe uli ndi anthu oposera 1 […]

Mtsogoleri  wa mpingo wa katolika pa dziko lonse, Papa Francisco  wapempha achinyamata kuti azikhala ndi masomphenya komanso njira zothekera  kukwaniritsa maso mphenya awo. Malipoti a wailesi ya Vatican ati Papa wanena izi pamene anayendera  achinyamata omwe ali mu bungwe la The Scholas Occurrentes ku Rome mdziko la Italy. Bungweli linakhazikitsidwa ndi Papa Francisco   m`dziko la […]

Golf Fundraising Tournament Coming Soon!!


Current track
Title
Artist