Contact us

P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 608/627/602/617
Fax (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

Anthu Khumi Ndi Asanu (15) Afa Mu Mzinda Wa Nairobi. 

 

Anthu khumi ndi asanu afa nyumba ina itawagwera usiku wa lolemba mu mzinda wa Nairobi mdziko la Kenya.

Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC bungwe la Kenya Red Cross lati anthu omwe amathandiza anthu pangozi zosiyanasiyana anafika kumalowa kukathandiza ena mwa anthuwo.

Malipoti ena ati anthu mazanamazana anakwanitsa kutuluka  nyumbamo pa nthawi ya ngozi-yi.

M’mwezi wa April chaka chino anthu enanso oposera makumi anayi anfa mu mzinda wa Nairobi mdzikomo nyumba ina itawagweranso.

 

On Air Studio Phone Numbers

Mobile App

Android devices
 
Apple devices
 
Windows Phone devices