Photo Gallery

Dedza Transmitter

Programme Schedule

Contact us

Radio Maria Malawi
P.O. Box 408,
Mangochi,
MALAWI.

Tel. (265) 01 599 605 /607 /608 /626/627
Fax. (265) 01 599 691
E-mail: radiomaria@africa-online.net

WFRM Newsletter

Welcome

RADIO MARIA is a broadcasting initiative, which was started in Italy by a group of Catholics, both priests and lay people. It aims at spreading the Good News of Jesus Christ to all people of good will. The radio is not commercially funded through advertisement, but lives solely by means of the generous donations of its listeners and the contributions of its volunteers.

On Radio Maria Malawi website you can listen to our live broadcast by clicking on the Live & Direct icon on the right hand side. You can also listen to recorded Ulaliki and music by going to the Media menu.

Please take the time to make a small donation to help us evangelise to poor souls. May God bless you all.

Nkhani ndi Zochitika

  • 22 July 2014
    Episkopi wa dayosizi ya Karonga ya mpingo wa katolika Ambuye Martin Mtumbuka omwe akuchita nawo msonkhano wa bungwe la Association of Member Episcopal Conferences in Eastern Africa (AMECEA) mumzinda wa Lilongwe ati sukulu za ukachenjede za mpingo wa katolika zili ndi udindo waukulu wolimbikitsa ntchito zamakono zofalitsira mawu a Mulungu. Poyankhula pamene amapereka phunziro lawo lokhudza magawo omwe sukulu za ukachenjede zili nawo pa ntchito zamakono zofalitsira uthenga wabwino pamsonkhano wa ...
  • 22 July 2014
    Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Fransisko wafunira mafuno abwino nthumwi za ku nsonkhano wa atsogoleri a mpingowu mdera la AMECEA omwe uli mkati ku Bingu International Conference Center mumzinda wa Lilongwe. Nduna ya Papa m’maiko a Malawi ndi Zambia Akiepiskopi Julio Murrat ndi omwe anapereka uthenga wa Papa Fransisko pa mwambo wa msembe ya misa yotsekulira msonkhanowu yomwe inachitikira ku bwalo la za masewero la CIVO mumzinda wa Lilongwe. “Ndikuyamika Mulungu chifukwa ...
  • 22 July 2014
    Akiepiskopi wa Akidayosizi ya Lilongwe Ambuye Tarcisius Ziyaye athokoza mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransisko chifukwa chowapatsa Pallium yatsopano chomwe ndi chizindikiro chowonetsa kutumidwa ndi Papa. Pallium ndi chovala chokolekera chomwe Papa amachipereka kwa Akiepiskopi yemwe wamutumidwa kukatumikira mu Akidayosizi ina. Ambuye Ziyaye pamodzi ndi Akiepiskopi Thomas Luke Msusa, Akiepiskopi wa Akidayosizi ya Blantyre anali mgulu la ma Akiepiskopi a m’maiko ...